Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 3:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemonso akabwerera wolungama kuleka cilungamo cace, ndi kucita cosalungama, ndipo ndikamuikira comkhumudwitsa, adzafa; popeza sunamcenjeza, adzafa m'cimo lace, ndi zolungama zace adazicita sizidzakumbukika; koma mwazi wace ndidzaufuna pa dzanja lako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:20 nkhani