Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinamva mkokomo wa mapiko a zamoyozo pakukhudzana, ndi mlikiti wa njingazo m'mbali mwa izo, ndilo phokoso la mkokomo waukuru.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 3

Onani Ezekieli 3:13 nkhani