Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 29:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakutaya kucipululu, iwe ndi nsomba zonse za m'mitsinje mwako; udzagwa kuthengo koyera, sudzaunjikidwa, kapena kuoledwa; ndakupereka ukhale cakudya ca zirombo za padziko, ndi mbalame za kumlengalenga,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 29

Onani Ezekieli 29:5 nkhani