Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 28:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwa mphulupulu zako zocuruka ndi malonda ako osalungama waipsa malo ako opatulika; cifukwa cace ndaturutsa moto m'kati mwako wakunyeketsa iwe; ndipo ndakusandutsa mapulusa panthaka pamaso pa onse akuona.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 28

Onani Ezekieli 28:18 nkhani