Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 28:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Unali m'Edene, munda wa Mulungu, mwala uli wonse wa mtengo wace unali copfunda cako, sardiyo, topazi, diamondi, berulo, sohamu, ndi yaspi, safiro, nofeki, bareketi, ndi golidi; malingaka ako ndi akazi ako anakutumikira tsiku lolengedwa iwe zinakonzekeratu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 28

Onani Ezekieli 28:13 nkhani