Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 27:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amalonda a ku Seba ndi a ku Rama anagulana nawe malonda; anagula malonda ako ndi zonunkhira zoposa ziri zonse, ndi miyala iri yonse ya mtengo wace, ndi golidi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27

Onani Ezekieli 27:22 nkhani