Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 27:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu a ku Dedani anakutsatsa malonda, zisumbu zambiri zinazolowerana nawe malonda ako, anabwera nazo minyanga ndi phingo kugulana nawe malonda.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 27

Onani Ezekieli 27:15 nkhani