Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 25:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Taona ndidzatambasulira Afilisti dzanja langa, ndi kulikha. Akereti, ndi kuononga otsalira mphepete mwa nyanja.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 25

Onani Ezekieli 25:16 nkhani