Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 24:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo uukhazike pa makara ace opanda kanthu m'menemo, kuti utenthe, nuyake mkuwa wace; ndi kuti codetsa cace cisungunuke m'mwemo, kuti dzimbiri lace lithe.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 24

Onani Ezekieli 24:11 nkhani