Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 22:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Waparamula nao mwazi wako, waukhetsa, nudetsedwa nao mafano ako udawapanga, nuyandikizitsa masiku ako, wafikiranso zako zako; cifukwa cace ndakuika ukhale citonzo ca amitundu ndi coseketsa ca maiko onse.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 22

Onani Ezekieli 22:4 nkhani