Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 22:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Ndipo ndinafunafuna munthu pakati pao wakumanganso linga, ndi kuimira dziko popasukira pamaso panga, kuti ndisaliononge; koma ndinapeza palibe.

31. Cifukwa cace ndinawatsanulira ukali wanga, ndawatha ndi moto wa kuzaza kwanga, njira yao yao ndinaibweza pa mutu pao, ati Ambuye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 22