Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 21:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Popeza mwakumbutsa mphulupulu yanu pobvumbuluka zolakwa zanu, kotero kuti macimo anu aoneka m'zonse muzicita, popeza mukumbukika, mudzagwidwa ndi dzanja.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21

Onani Ezekieli 21:24 nkhani