Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 21:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pfuula ndi kulira, wobadwa ndi munthu iwe, pakuti likhalira pa anthu anga, likhalira pa akalonga onse a Israyeli, laperekedwa kulupanga pamodzi ndi anthu anga; cifukwa cace panda pancafu pako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21

Onani Ezekieli 21:12 nkhani