Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 21:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti,

2. Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako ku Yerusalemu, nuwabenthulire mau malo opatulikawa, nunenere dziko la Israyeli kulitsutsa;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21