Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 20:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nuziti kwa nkhalango ya kumwera kwa Yuda, Tamvera mau a Yehova, Atero Ambuye Yehova, Taona ndidzayatsa moto mwa iwe, udzanyeketsa mtengo uli wonse wauwisi mwa iwe, ndi mtengo uli wonse wouma; malawi amoto sadzazimika, ndi nkhope zonse kuyambira kumwera kufikira kumpoto zidzapsa nao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:47 nkhani