Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 20:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti pa phiri langa lopatulika, pa phiri lothubvuka la Israyeli, ati Ambuye Yehova, pomwepo onse a nyumba ya Israyeli, onsewo adzanditumikira Ine m'dzikomo; pomwepo ndidzawalandira, ndi pomwepo ndidzafuna nsembe zanu zokweza, ndi zoyamba za msonkho wanu, pamodzi ndi zopatulika zanu zonse.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:40 nkhani