Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 20:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anawo anapandukira Ine, sanayenda m'malemba anga, kapena kusunga maweruzo anga kuwacita, amene munthu akawacita adzakhala nao ndi moyo; anaipsa masabata anga; pamenepo ndinati ndidzawatsanulira ukali wanga, kuwakwaniritsira mkwiyo wanga m'cipululu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:21 nkhani