Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 20:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma nyumba ya Israyeli inapaodukira Ine m'cipululu, sanayenda m'malemba anga, nanyoza maweruzo anga, amene, munthu akawacita adzakhala nao ndi moyo; ndi masabata anga anawaipsa kwambiri; pamenepo ndidati ndiwatsanulire ukali wanga m'cipululu kuwatha.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:13 nkhani