Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 18:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma woipayo akabwerera kusiya macimo ace onse adawacita nakasunga malemba anga onse, ndi kucita ciweruzo ndi cilungamo, adzakhala ndi moyo ndithu, sadzafa.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 18

Onani Ezekieli 18:21 nkhani