Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 16:52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usenzenso manyazi ako, iwe wakuweruza abale ako mwa zocimwa zako unazicita monyansa koposa iwowa; iwo akuposa iwe m'cilungamo cao, nawenso ucite manyazi nusenze manyazi ako, popeza waika abale ako olungama.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16

Onani Ezekieli 16:52 nkhani