Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 16:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Popeza sunakumbukila masiku a ubwana wako, koma wandibvuta nazo zonsezi, cifukwa cace taona, Inenso ndidzakubwezera njira yako pamutu pako, ati Ambuye Yehova; ndipo sudzacita coipa ici coonjezerapo pa zonyansa zako zonse.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16

Onani Ezekieli 16:43 nkhani