Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 14:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace uziti kwa nyumba ya Israyeli, Atero Ambuye Yehova, Bwerani, lekani mafano anu, tembenuzani nkhope zanu kuzisiya zonyansa zanu zonse.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 14

Onani Ezekieli 14:6 nkhani