Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 13:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi dzanja langa lidzakhala lotsutsana nao aneneri akuona zopanda pace, ndi kupenda za bodza; sadzakhala mu msonkhano wa anthu anga, kapena kulembedwa m'buku lolembedwamo nyumba ya Israyeli, kapena kulowa m'dziko la Israyeli; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Ambuye Yehova,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 13

Onani Ezekieli 13:9 nkhani