Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 13:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace simudzaonanso zopanda pace, kapena kupenda; koma ndidzalanditsa anthu anga m'manja mwanu; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 13

Onani Ezekieli 13:23 nkhani