Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 12:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace uziti nao, Atero Ambuye Yehova, Palibe amodzi a mau anga adzazengerezekanso; koma mau ndidzanenawo adzacitika, ati Ambuye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 12

Onani Ezekieli 12:28 nkhani