Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 12:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kalongayo ali pakati pao adzasenza paphewa pace mumdima, nadzaturuka; adzaboola palinga, nadzaturutsapo; adzaphimba nkhope yace kuti asapenye dziko ndi maso ace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 12

Onani Ezekieli 12:12 nkhani