Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 11:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wobadwa ndi munthu iwe, abale ako, inde abale ako amuna a cibale cako, ndi nyumba yonse ya Israyeli, yonseyi ndiwo amene okhala m'Yerusalemu ananena nao, Muzikhala kutali kwa Yehova; dziko ili lapatsidwa kwa ife, likhale colowa cathu;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 11

Onani Ezekieli 11:15 nkhani