Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 10:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinapenya, ndipo taonani, njinga zinai m'mbali mwa akerubi, njinga imodzi m'mbali mwa kerubi mmodzi, ndi njinga yina m'mbali mwa kerubi wina, ndi maonekedwe a njingazi ananga mawalidwe a berulo.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 10

Onani Ezekieli 10:9 nkhani