Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 1:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Poyenda zija zinayenda izi, poima zija zinaima izi; ndipo ponyamuka pansi zija njingazi zinanyamuka pambali pa izo; pakuti mzimu wa zamoyozo unali mu njingazi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1

Onani Ezekieli 1:21 nkhani