Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 1:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mafaniziro a nkhope zao zinali nayo nkhope ya munthu; ndi izi zinai zinali nayo nkhope ya mkango pa mbali ya ku dzanja lamanja; ndi izi zinai zinali nayo nkhope ya ng'ombe pa mbali ya ku dzanja lamanzere; izi zinai zinali nayonso nkhope ya ciombankhanga.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1

Onani Ezekieli 1:10 nkhani