Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 8:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapereka malamulo a mfumu kwa akazembe a mfumu, ndi kwa ziwanga, tsidya lino la mtsinjewo; ndipo iwo anathandiza anthu ndi nyumba ya Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Ezara 8

Onani Ezara 8:36 nkhani