Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 8:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero ansembe ndi Alevi analandira kulemera kwace kwa siliva ndi golidi ndi zipangizo, abwere nazo ku Yerusalemu ku nyumba ya Mulungu wathu.

Werengani mutu wathunthu Ezara 8

Onani Ezara 8:30 nkhani