Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 8:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinawasonkhanitsa ku mtsinje wopita ku Ahava, ndi komweko tinakhala m'misasa masiku atatu; ndipo ndinapenyerera anthu ndi ansembe, koma sindinapezapo wa ana a Levi.

Werengani mutu wathunthu Ezara 8

Onani Ezara 8:15 nkhani