Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 7:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti tsiku loyamba la mwezi woyamba, ndilo ciyambi ca ulendo wokwera kucokera ku Babulo, ndi tsiku lacimodzi la mwezi wacisanu anafika ku Yerusalemu, monga linamkhalira dzanja lokoma la Mulungu wace.

Werengani mutu wathunthu Ezara 7

Onani Ezara 7:9 nkhani