Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ezara amene anakwera kucokera ku Babulo, ndiye mlembi waluntha m'cilamulo ca Mose, cimene Yehova Mulungu wa Israyeli adacipereka; ndipo mfumu inampatsa copempha iye conse, monga linamkhalira dzanja la Yehova Mulungu wace.

Werengani mutu wathunthu Ezara 7

Onani Ezara 7:6 nkhani