Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 7:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ine Aritasasta, mfumu ine, ndilamulira osunga cuma onse okhala tsidya lija la mtsinjewo, kuti ciri conse akupemphani Ezara wansembe, mlembi wa lamulo la Mulungu wa Kumwamba, cicitike mofulumira;

Werengani mutu wathunthu Ezara 7

Onani Ezara 7:21 nkhani