Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 6:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi zipangizo za golidi ndi siliva za nyumba ya Mulungu, zimene anaziturutsa Nebukadinezara m'Kacisi ali ku Yerusalemu, nazitenga kumka nazo ku Babulo, azibwezere, nabwere nazo ku Kacisi ali ku Yerusalemu, ciri conse ku malo ace; naziike m'nyumba ya Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Ezara 6

Onani Ezara 6:5 nkhani