Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 6:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo popatulira nyumba iyi ya Mulungu anapereka ng'ombe zana limodzi, nkhosa zamphongo mazana awiri, ana a nkhosa mazana anai, ndi za nsembe yazolakwa ya Aisrayeli onse atonde khumi ndi awiri, monga mwa kuwerenga kwace kwa mapfuko a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Ezara 6

Onani Ezara 6:17 nkhani