Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 6:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Mulungu wokhalitsa dzina lace komweko agwetse mafwnu onse ndi mitundu yonse ya anthu, akuturutsa dzanja lao kusintha mau awa, kuononga nyumba ya Mulungu iri ku Yerusalemu. Ine Dariyo ndalamulira, cicitike msanga.

Werengani mutu wathunthu Ezara 6

Onani Ezara 6:12 nkhani