Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 5:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adziwe mfumu kuti ife tinamuka ku dziko la Yuda, ku nyumba ya Mulungu wamkuru, yomangidwa ndi miyala yaikuru, niikidwa mitengo pamakoma, nicitika mofulumira nchitoyi, nikula m'dzanja mwao.

Werengani mutu wathunthu Ezara 5

Onani Ezara 5:8 nkhani