Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 5:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Zerubabele mwana wa Sealitiyeli, ndi Yesuwa mwana wa Yozadaki, ananyamuka, nayamba kumanga nyumba ya Mulungu iri ku Yerusalemu, anali pamodzi nao aneneri a Mulungu akuwathandiza.

Werengani mutu wathunthu Ezara 5

Onani Ezara 5:2 nkhani