Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 5:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsono cikakomera mfumu, munthu asanthule m'nyumba ya cuma ca mfumu iri komwe ku Babulo, ngati nkuterodi, kuti Koresi mfumu analamulira kuti azimanga nyumba iyi ya Mulungu ku Yerusalemu; ndipo mfumu ititumizire mau omkomera pa cinthuci.

Werengani mutu wathunthu Ezara 5

Onani Ezara 5:17 nkhani