Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 5:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso zipangizo za golidi ndi siliva za nyumba ya Mulungu, anaziturutsa Nebukadinezara m'Kacisi anali ku Yerusalemu, ndi kubwera nazo ku kacisi wa ku Babulo, izizo Koresi mfumu anaziturutsa m'kacisi wa ku Babulo, nazipereka kwa munthu dzina lace Sezibazara, amene anamuika akhale kazembe;

Werengani mutu wathunthu Ezara 5

Onani Ezara 5:14 nkhani