Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma makolo athuwo atautsa mkwiyo wa Mulungu wa Kumwamba, Iye anawapereka m'dzanja la Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo Mkasidi, amene anaononga nyumba yino, natenga anthu ndende kumka nao ku Babulo.

Werengani mutu wathunthu Ezara 5

Onani Ezara 5:12 nkhani