Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 2:28-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

28. Anthu a ku Beteli ndi Ai, mazana awiri mphambu makumi awiri kudza atatu.

29. Ana a Nebo, makumi asanu mphambu awiri.

30. Ana a Magabisi, zana limodzi mphambu makumi asanu kudza asanu ndi mmodzi.

31. Ana a Elamu wina, cikwi cimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi asanu ndi anai.

Werengani mutu wathunthu Ezara 2