Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 10:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Ezara ananyamuka pakhomo pa nyumba ya. Mulungu, nalowa m'cipinda ca Yehohanana mwana wa Eliyasibu, ndipo atafikako sanadya mkate, sanamwa madzi; pakuti anacita maliro cifukwa ca kulakwa kwa iwo otengedwa ndende.

Werengani mutu wathunthu Ezara 10

Onani Ezara 10:6 nkhani