Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 1:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Koresi mfumu ya ku Perisiya, Yehova Mulungu Wam'mwamba anandipatsa maufumu onse a pa dziko lapansi, nandilangiza ndimmangire nyumba m'Yerusalemu, ndiwo m'Yuda.

Werengani mutu wathunthu Ezara 1

Onani Ezara 1:2 nkhani