Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 9:31-32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. kukhazikitsa masiku awa a Purimu m'nyengo zao, m'mene Moredekai Myuda ndi mkazi wamkuru Estere adawakhazikitsira; ndi umo anadzikhazikitsira okha, ndi mbeu yao, kunena za kusala kwao, ndi kupfuula kwao.

32. Ndipo kunena kwace kwa Estere kunakhazikitsa mau awa a Purimu; ndipo kunalembedwa m'buku.

Werengani mutu wathunthu Estere 9