Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 9:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kuti masikuwa adzakumbukika ndi kusungika mwa mibadwo yonse, banja liri lonse, dziko liri lonse, ndi mudzi uli wonse; ndi kuti masiku awa sadzalekeka mwa Ayuda, kapena kusiyidwa cikumbukilo cao mwa mbeu yao.

Werengani mutu wathunthu Estere 9

Onani Estere 9:28 nkhani