Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 8:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati, Cikakomera mfumu, ndipo ngati yandikomera mtima, niciyenera kwa mfumu, ngatinso ndimcititsa kaso, alembere cosintha mau a akalata a ciwembu ca Hamani mwana wa Hamedata wa ku Agagi, amene adawalembera kuononga Ayuda okhala m'maiko onse a mfumu;

Werengani mutu wathunthu Estere 8

Onani Estere 8:5 nkhani